Mateyu 26:64 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu anati kwa iye, Mwatero, koma ndinenanso kwa inu, 5 Kuyambira tsopano mudzaona Mwana wa munthu ali kukhala ku dzanja lamanja la mphamvu, ndi kufika pa mitambo ya kumwamba.

Mateyu 26

Mateyu 26:62-68