Mateyu 26:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Iye, Mukani kumzinda kwa munthu wangana, mukati kwa iye, Mphunzitsi anena. Nthawi yanga yayandikirai ndidzadya Paskha kwanu pamodzi ndi ophunzira anga.

Mateyu 26

Mateyu 26:8-22