Mateyu 26:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku loyamba la mkate wopanda cotupitsa, ophunzira anadza kwa Yesu, nati, Mufuna tikakonzere kuti Paskha, kuti mukadye?

Mateyu 26

Mateyu 26:12-18