Mateyu 25:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Iye adzayankha iwo kuti, Indetu ndinena kwa inu, Cifukwa munalibe kucitira ici mmodzi wa awa ang'onong'ono, munalibe kundicitira ici Ine.

Mateyu 25

Mateyu 25:35-46