Mateyu 25:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndinali mlendo, ndipo simunandilandira Ine; wamarisece ndipo simunandibveka Ine; wodwala, ndi m'nyumba yandende, ndipo simunadza kundiona Ine.

Mateyu 25

Mateyu 25:36-46