Mateyu 25:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Ufumu wa Kumwamba udzafanizidwa ndi anamwali khumi, amene anatenga nyali zao, naturuka kukakomana ndi mkwati.

Mateyu 25

Mateyu 25:1-5