Mateyu 24:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Iye anayankha nati kwa iwo, Simuona izi zonse kodi? indetu ndinena kwa inu, Sipadzakhala pano mwala umodzi pa unzace, umene sudzagwetsedwa.

Mateyu 24

Mateyu 24:1-5