Mateyu 24:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anaturuka kuKacisi; ndipo ophunzira ace anadza kudzamuonetsa cimangidwe ca Kacisiyo.

Mateyu 24

Mateyu 24:1-5