Mateyu 23:7-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

7. ndi kulankhulidwa m'misika, ndi kuchedwa ndi anthu, Rabi.

8. Koma inu musachedwa Rabi; pakuti Mphunzitsi wanu ali mmodzi, ndipo inu nonse muli abale.

9. Ndipo inu musachule wina atate wanu pansi pano, pakuti alipo mmodzi ndiye Atate wanu wa Kumwamba.

10. Ndipo musachedwa atsogoleri, pakuti alipo mmodzi Mtsogoleri wanu, ndiye Kristu.

Mateyu 23