Mateyu 21:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nanena kwa Iye, Mulinkumva kodi cimene alikunena awa? Ndipo Yesu ananena kwa iwo, Inde: simunawerenga kodi, M'kamwa mwa makanda ndi oyamwa munafotokozera zolemekeza?

Mateyu 21

Mateyu 21:9-21