Mateyu 21:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ansembe akuru ndi alembi, m'mene anaona zozizwitsa zomwe Iye anazicita, ndi ana alinkupfuula kuKacisiko kuti, Hosana kwa Mwana wa Davide, anapsa mtima,

Mateyu 21

Mateyu 21:6-24