Mateyu 20:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yesu anayankha nati, Inu simudziwa cimene mupempha, Kodi mukhoza kumwera cikho nditi ndidzamwere Ine? Iwo ananena kwa Iye, Ife tikhoza.

Mateyu 20

Mateyu 20:15-32