Mateyu 20:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anati kwa iye, Ufuna ciani? Iye ananena, Lamulirani kuti ana anga awiri amenewa adzakhale, wina ku dzanja lanu lao manja, ndi wina kulamanzere, mu ufumu wanu.

Mateyu 20

Mateyu 20:16-25