Mateyu 2:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nawatumiza ku Betelehemu, nati, Yendani mufunitsitse za kamwanako; ndipo pamene mudzampeza, mundibwezere mau, kuti inenso ndidzadze kudzamlambira Iye.

Mateyu 2

Mateyu 2:2-15