Mateyu 18:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu ananena kwa iye, Sindinena kwa iwe kufikira kasanu ndi kawiri, koma kufikira makumi ananu ndi awiri kubwerezedwa kasanu ndi kawiri.

Mateyu 18

Mateyu 18:14-23