Mateyu 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Petro anadza, nati kwa Iye, Ambuye, mbale wanga adzandilakwira kangati, ndipo ine ndidzamkhululukira iye? kufikira kasanu ndi kawiri kodi?

Mateyu 18

Mateyu 18:12-29