Mateyu 17:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akali cilankhulire, onani, mtambo wowala unawaphi mba iwo: ndipo onani, mau alikunena mumtambo, Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, mwa iyeyu ndikondwera, mverani Iye.

Mateyu 17

Mateyu 17:1-12