Mateyu 17:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Petro anayankha, nati kwa Yesu, Ambuye, kuli bwino kuti ife tikhale pano; ngati mulola ndidzamanga pane misasa itatu; umodzi wa Inu, ndi wina wa Mose, ndi wina wa Eliya.

Mateyu 17

Mateyu 17:1-8