Mateyu 16:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Iye anapotoloka, nati kwa Petro, Pita kumbuyo kwanga, Satana iwe; ndiwe condikhumudwitsa Ine; cifukwa sumasamalira za Mulungu, koma za anthu.

Mateyu 16

Mateyu 16:16-25