Mateyu 16:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzakupatsa mafungulo a Ufumu wa Kumwamba; ndipo cimene ukamanga pa dziko lapansi cidzakhala comangidwa Kumwamba: ndipo cimene ukacimasula pa dziko lapansi, cidzakhala comasulidwa Kumwamba.

Mateyu 16

Mateyu 16:14-25