Mateyu 14:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene panali madzulo, ophunzira ace anafika kwa Iye, nanena, Malo ano nga cipululu, ndipo nthawi yapita tsopano; kauzeni makamuwo amuke, apite ku midzi kukadzigulira okha kamba.

Mateyu 14

Mateyu 14:12-23