Mateyu 14:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anaturuka, naona khamu lalikuru la anthu, nacitira iwo cifundo, naciritsa akudwala ao.

Mateyu 14

Mateyu 14:8-20