Mateyu 13:52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anati kwa iwo, Cifukwa cace, mlembi ali yense, wophunzitsidwa mu Ufumu wa Kumwamba, ali wofanana ndi munthu mwini banja, amene aturutsa m'cuma cace zinthu zakale ndi zatsopano.

Mateyu 13

Mateyu 13:42-53