Mateyu 13:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye amene afesedwa pa nthaka yabwino, uyu ndiye wakumva mau nawadziwitsa; amene abaladi zipatso, nazifitsa, ena za makumi khumi, ena za makumi asanu ndi limodzi, ena za makumi atatu.

Mateyu 13

Mateyu 13:22-33