Mateyu 13:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye amene afesedwa kuminga, uyu ndiye wakumva mau; ndipo kulabadira kwa dziko lapansi, ndi cinyengo ca cuma citsamwitsa mau, ndipo akhala wopanda cipatso.

Mateyu 13

Mateyu 13:19-28