Mateyu 12:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo ananena Iye kwa munthuyo, Tansa dzanja Lako. Ndipo iye analitansa, ndipo linabwezedwa lamoyo longa linzace.

Mateyu 12

Mateyu 12:3-19