Mateyu 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Iye anadziitanira ophunzira ace khumi ndi awiri, anapatsa iwo mphamvu pa mizimu yoipa, yakuiturutsa, ndi yakuciza nthenda iri yonse ndi zofoka zonse.

Mateyu 10

Mateyu 10:1-4