Masalmo 98:8-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Mitsinje iombe manja;Mapiri apfuule pamodzi mokondwera; Pamaso pa Yehova, popeza akudza kudzaweruza dziko