Masalmo 91:6-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Kapena mliri woyenda mumdima,Kapena cionongeko cakuthera usana.

7. Pambali pako padzagwa cikwi,Ndi zikwi khumi pa dzanja lamanja lako;Sicidzakuyandikiza iwe.

8. Koma udzapenya ndi maso ako,Nudzaona kubwezera cilango oipa.

9. Popeza udati, Inu Yehova, ndinu pothawirapo pangaUdaika Wam'mwambamwamba cokhalamo cako;

Masalmo 91