Masalmo 82:7-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

7. Komatu mudzafa monga anthu,Ndipo mudzagwa monga wina wa akulu.

8. Ukani, Mulungu, weruzani dziko lapansi;Pakuti Inu mudzalandira amitundu onse.

Masalmo 82