Masalmo 67:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Aticitire cifundo Mulungu, ndi kutidalitsa,Atiwalitsire nkhope yace;

2. Kuti njira yanu idziwike pa dziko lapansi,Cipulumutso canu mwa amitundu onse.

Masalmo 67