Masalmo 61:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Imvani mpfuu wanga, Mulungu;Mverani pemphero langa.

2. Ku malekezero a dziko lapansi ndidzapfuulira kwa Inu, pomizika mtima wanga:Nditsogolereni ku thanthwe londiposa ine m'kutalika kwace.

3. Pakuti munakhala pothawirapo panga; nsanja yolimba pathawa mdani ine.

Masalmo 61