Masalmo 57:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Ndidzakuyamikirani mwa anthu, Ambuye:Ndidzakuyimbirani mwa mitundu.

10. Pakuti cifundo canu ncacikuru kufikira m'mwamba,Ndi coonadi canu kufikira mitambo.

11. Kwezekani m'mwambamwamba, Mulungu;Ulemerero wanu ukhale pamwamba m'dziko lonse lapansi.

Masalmo 57