Masalmo 56:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mwalanditsa moyo wanga kuimfa:Simunatero nao mapazi anga kuti ndingagwe?Kuti ndiyende pamaso pa MulunguM'kuunika kwa amoyo.

Masalmo 56

Masalmo 56:11-13