Masalmo 57:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mundicitire cifundo, Mulungu, mundicitire cifundo;Pakuti moyo wanga ukhulupirira Inu:Ndipo ndithawira ku mthunzi wa mapiko anu,Kufikira zosakazazo zidzapita.

Masalmo 57

Masalmo 57:1-9