Masalmo 56:6-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Amemezana, alalira,Achereza mapazi anga,Popeza alindira moyo wanga.

7. Kodi adzapulumuka ndi zopanda pace?Gwetsani anthu mumkwiyo, Mulungu.

8. Muwerenga kuthawathawa kwanga:Sungani misozi yanga m'nsupa yanu;Kodi siikhala m'buku mwanu?

Masalmo 56