Masalmo 54:6-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Ine mwini ndidzapereka nsembe kwa Inu:Ndidzayamika dzina lanu, Yehova, pakuti nlokoma.

7. Pakuti anandilanditsa m'nsautso yonse;Ndipo ndapenya ndi diso langa ico ndakhumbira pa adani anga,

Masalmo 54