Masalmo 35:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anandichera ukonde wao m'mbunamo kopanda cifukwa,Anakumbira moyo wanga dzenje kopanda cifukwa.

Masalmo 35

Masalmo 35:5-17