Masalmo 22:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Mbumba ya anthu idzamtumikira;Kudzanenedwa za Ambuye ku mibadwo yakudza.

31. Iwo adzadza nadzafotokozera cilungamo caceKwa anthu akadzabadwa, kuti Iye anacicita.

Masalmo 22