Masalmo 22:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndathiridwa pansi monga madzi,Ndipo mafupa anga onse anaguluka:Mtima wanga ukunga sera; Wasungunuka m'kati mwa matumbo anga,

Masalmo 22

Masalmo 22:12-21