Masalmo 143:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mundimvetse cifundo canu mamawa;Popeza ndikhulupirira Inu:Mundidziwitse njira ndiyendemo;Popeza ndikweza moyo wanga kwa Inu.

Masalmo 143

Masalmo 143:3-12