Masalmo 136:3-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Yamikani Mbuye wa ambuye:Pakuti cifundo cace ncosatha.

4. Amene yekha acita zodabwiza zazikuru:Pakuti cifundo cace ncosatha.

5. Amene analenga zakumwamba mwanzeru:Pakuti cifundo cace ncosatha.

6. Amene anayala dziko lapansi pamwamba pa madzi:Pakuti cifundo cace ncosatha.

Masalmo 136