Masalmo 136:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Napititsa Israyeli pakati pace;Pakuti cifundo cace ncosatha.

15. Nakhutula Farao ndi khamu lace m'Nyanja Yofiira:Pakuti cifundo cace ncosatha.

16. Amene anatsogolera anthu ace m'cipululu:Pakuti cifundo cace ncosatha.

Masalmo 136