Masalmo 102:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anapenya pansi ali kumwamba kuli malo ace opatulika;Yehova pokhala kumwamba anapenya dziko lapansi;

Masalmo 102

Masalmo 102:17-22