Marko 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye ananena nao, Yesaya ananenera bwino za inu onyenga, monga mwalembedwa,Anthu awa andilemekeza Ine ndi milomo yao,Koma mtima wao ukhala kutari ndi ine.

Marko 7

Marko 7:1-13