Marko 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo pakucoka kumsika, sakudya osasamba m'thupi; ndipo ziripo zinthu zina zambiri anazilandira kuzisunga, ndizo matsukidwe a zikho, ndi miphika, ndi zotengera zamkuwa.

Marko 7

Marko 7:1-14