Marko 4:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo ofesedwa pa nthaka yabwino ndiwo oterewa akumva mau, nawalandira, nabala zipatso zakupindula makumi atatu, ndi makumi asanu ndi limodzi, ndi makumi khumi.

Marko 4

Marko 4:11-23