Marko 15:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

anadzapo Y osefe wa ku Arimateya, mkulu wa mirandu womveka, amene yekha analikuyembekezera Ufumu wa Mulungu; nalimba mtima nalowa kwa Pilato, napempha mtembo wace wa Yesu.

Marko 15

Marko 15:34-47