Marko 10:2-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Ndipo anadza kwa Iye Afarisi, namfunsa Iye ngati kuloledwa kuti munthu acotse mkazi wace, namuyesa Iye.

3. Ndipo Iye anayankha nati kwa iwo, Kodi Mose anakulamulirani ciani?

4. Ndipo anati, Mose analola kulembera kalata wakulekanira, ndi kumcotsa.

Marko 10