Marko 9:50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mcere uli wabwino; koma ngati mcere unasukuluka, mudzaukoleretsa ndi ciani? Khalani nao mcere mwa inu nokha, ndipo khalani ndi mtendere wina ndi mnzace.

Marko 9

Marko 9:48-50